M’modzi mwa oyimba akazi omwe agwira nsewu pano, Tunosiwe Mwakalinga, yemwe amadziwika kwambiri ndi dzina loti Tuno, wadandaula kuti amakhomeleledwa ndi oyimba anzake ndipo waulula kuti woyimba Fireboy anaonetsa chidwi choyimba naye koma wati woyimba wina kumpanje kuno anatchingira. Woyimbayu wayankhula izi kudzera pa tsamba lake la nchezo la X lija kale linkatchedwa Twitter, pomwe […]
The post Anthu amandikhomelera, anamusowetsa Fireboy akufuna kuyimba nane – walira mokweza Tuno appeared first on Malawi 24.