..akuti Nankhumwa amafuna awakhomelele A Malawi oposa 200 omwe anali paulendo aja, afika m’dziko la Israel ndipo ati ndiokozeka kukhala ma tenanti koma akutitu ukuku kuli nyumba zosanjikizana mbwelekete ndipo akuti kuno ku mpanje timangonamizana pa nkhani ya mamangidwe komaso ati anakakonda a Lazarus Chakwera anakapita nawo kuti akaone mamangidwe apamwambawo. Ndege yomwe yanyamula anthuwa […]
The post Anthu aja afika ku Israel, akuti kuno za mamangidwe timangonamizana appeared first on Malawi 24.