ABungwe la achialubino la Association of People Living with Albinism in Malawi (Apam) lati likuda nkhawa ndi chisankho chikubwerachi chifukwa ndi nthawi yomwe amachitiridwa nkhanza kapena kuphedwa kumene. Mkulu wa bungweli a Young Muhamba ndiwo adandaula izi poyankhapo pa nkhani ya manda a munthu wachialubino omwe anafukulidwa ku Mulanje. Apolisi m’boma la Mulanje akufunafuna anthu […]
The post Anthu achialubino adandaula kuti akumaphedwa kwambiri nthawi yachisankho ikayandikira appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.