Anthu abwere adzafufuze okha – Zomba mental yakana kuti ogwira ntchito akumachitira nkhaza, kupha odwala misala ozunguza

Akuluakulu pa chipatala cha anthu odwala matenda a misala ku Zomba awuza anthu m’dziko muno kuti ali ololedwa kupanga kafukufuku wawo-wawo pa mphekesera yoti ogwira ntchito ena pa chipatalachi akumazuza mpaka kupha odwala ozunguza pa nthawi yomwe apita ku chipatalachi kukalandira thandizo. Chatsitsa dzaye kuti njovu ithyoke nyanga nchakuti anthu m’masamba a nchezo akugawana nkhani […]

The post Anthu abwere adzafufuze okha – Zomba mental yakana kuti ogwira ntchito akumachitira nkhaza, kupha odwala misala ozunguza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください