Anthu a ku Dowa awonetsa chikondi pa mwana yemwe akupita ku Israel

Anthu pamasamba a mchezo ayamikira anthu a kwa Msakambewa ku Dowa chifukwa cha chikondi chomwe awonetsa pa mwana wa m’mudzi mwawo yemwe akukapitiriza maphunziro ku Israel. Anthu a kwa Msakambewa anatutana kupita ku bwalo lokwerera ndege la Kamuzu International kumuperekeza mwana wawoyi. Malingana ndi kanema yemwe akuyendayenda m’masamba a mchezo, anthuwa anasonkha ndalama yomwe amupasa […]

The post Anthu a ku Dowa awonetsa chikondi pa mwana yemwe akupita ku Israel appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください