Pomwe anthu ochuluka anayamba kuiwala za matenda a Covid-19, zadziwika kuti matendawa anakalipo mdziko muno pomwe ku Nsanje akuti anthu asanu ndi awiri (7), apezeka ndi kachirombo koyambitsa matendawa. Izi ndi malingana ndi a George Mbotwa omwe ndi m’modzi mwa akuluakulu ku ofesi ya zaumoyo m’boma la Nsanje omwe atsimikizira nyumba zina zofalitsa nkhani mdziko […]
The post Anthu 7 apezeka ndi kachirombo ka Covid-19 ku Nsanje appeared first on Malawi 24.