ANTHU 26,000 ALI NDI KACHILOMBO KA HIV KU NSANJE

Kafukufuku wa kufala kwa kachirombo ka HIV yemwe bungwe la MACRO linachita mb’oma la Nsanje, waonetsa kuti pali kukwera kwa chiwerengero cha anthu omwe atenga kachiromboka kuyambira mwezi July 2022 kufikira July 2023. Bungweli latinso matenda opatsirana pogonana akupitilira kukwera mb’omali. Ndipo pofuna kuthetsa vutoli bungwe la AlDS Health Foundation lakhala likupereka ma kondomu oposa […]

The post ANTHU 26,000 ALI NDI KACHILOMBO KA HIV KU NSANJE appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください