Anthu khumi ndi awiri, avulala pangozi yomwe inachitika ku Kanjedza-Blantyre pamene minibus yomwe adakwera inalowa mbali yolakwika ndikugunda galimoto ya mtundu wa Corolla isanagunde minibus inanso. Malinga ndi Mneneri wa Polisi ya Limbe, a Aubrey Singanyama, ngoziyi inachitika pafupi ndi malo omwetsela mafuta a Puma ku Blantyre ndipo minibus yomwe inachita ngoziyi imachoka mseu wa […]
The post Anthu 12 avulala pa ngozi ku Blantyre appeared first on Malawi 24.