Anjatwa kamba kakupha bambo ofuna ogwilira

Ku Monkey-Bay m’boma la Mangochi, abambo awiri ali m’manja mwa apolisi kamba kakupha bambo wina yemwe akuti anamugwira akufuna kugwililira mayi yemwe anali nyumba yake usiku. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Monkey Bay, Sergeant Alice Sichali omwe azindikira abambo awiriwa ngati a Oscar Lungwa a zaka 34 komaso a Uladi Frank […]

The post Anjatwa kamba kakupha bambo ofuna ogwilira appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください