Apolisi m’boma la Nkhotakota amanga mkulu wa za malonda ku Chidewe ADMARC, Patrick Duston wa zaka 35, pomuganizira kuti ndi amene anazembetsa matumba 124 achimanga a ndalama zomwana 7.3 miliyoni. Mneneri wa apolisi ya Nkhunga, Andrew Kamanga, wati apolisi analandira lipoti kuchokera ku likulu la ADMARC chigawo chapakati pa 10 February, 2024. “Lipoti likutsindika kuti […]
The post Anjatidwa kamba kozembetsa matumba 124 a chimanga ku ADMARC appeared first on Malawi 24.