Mayi wina wa zaka 24 zakubadwa m’boma la Nkhotakota watsekeledwa mchitokosi pa polisi ya Nkhunga kamba konyoza ndikutukwana apolisi kudzera pa tsamba lake la mchezo la Fesibuku. Mayiyu yemwe dzina lake ndi Anastasia Kamanga, adatukwakwana apolisi kuphatikizapo makolo awo omwe adabereka a polisiwa pa tsamba la mchezo lotchedwa Zokonda Amai Macheza pamene iye amkadzudzula apolisi […]
The post Anjatidwa kamba kotukwana apolisi patsamba la mchezo la Fesibuku appeared first on Malawi 24.