Apolisi ku Chileka mu mzinda wa Blantyre amanga bambo Paul Mugawa a zaka 50 zakubadwa powaganizira kuti amagonana ndi mtsikana wa za 14. Mneneri wa apolisi ya Chileka, Jonathan Phillipo, wati a Mugawa anali pa ubwenzi ndi mtsinakayu kuyambila mwezi wa October chaka chatha. A Phillipo anati :”Mai a mwanayu ndiye anadzapereka lipoti ku polisi […]
The post Anjatidwa kamba kogwililira mtsikana wa zaka 14 appeared first on Malawi 24.