Mneneri wa boma a Moses Kunkuyu apempha andale, atolankhani, anthu apa social media, komanso amipingo kuti asafune kutchuka pa nkhaniyi pokhala patsogolo kumafalitsa nkhani zobweresa kusiyana mdziko pamene ntchito yosanga ndege ili mkati. A Kunkuyu anena izi pomwe amachitisa msonkhano wa atolankhani mamawa uno pamodzi ndi mkulu wa asilikali a Valentino Phiri ku Lilongwe pa […]
The post ‘Andale, atolankhani, a mpingo tiyeni tisafune kutchukirapo pankhani ya kusowa kwa ndege’ appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.