Anandiyimitsa udindo popanda chifukwa: yadandula mfumu yaikulu Amidu ku Balaka

Mfumu yaikulu Amidu ya m’boma la Balaka yadandaula kuti akuluakulu a khonsolo ya Balaka adaiyimitsa pa udindo wa ufumu pa zifukwa zomwe sakuzidziwa. Poyankhula ndi Malawi24, mfumuyi, yomwe dzina lake lakubadwa ndi Amina Gayesi, yati kwa miyezi isanu ndi iwiri tsopano, iyo yakhala isakulabadilidwa mu misonkhano komanso zochitika zosiyanasiyana zokhudzana ndi khonsoloyi. ”Ndidalandira uthenga wakuti […]

The post Anandiyimitsa udindo popanda chifukwa: yadandula mfumu yaikulu Amidu ku Balaka appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください