Akatswiri pa nkhani zolosela nyengo m’dziko muno ati a Malawi ayembekezere kulandila mvula yochepa mwezi uno wa February moyerekeza ndi mwezi watha. Izi zanenedwa kudzera mu ulosi umene nthambi yoona za nyengo yatulutsa okhudza kagwede ka mvula mwezi uno. Malingana ndi a zanyengo, madera ambiri dziko muno ayembekezere kulandira ng’amba yochuluka. Ngakhale izi chili chomwechi, […]
The post Anamandwa olosela nyengo ati mwezi uno mvula ichepa kagwedwe kake appeared first on Malawi 24.