Kwavuta ku Soche Technical College ku Blantyre komwe ana a sukulu akutseka misewu kamba kokwiya kuti miyezi ikudusa koma akungolandira zakudya zomwe ndiwo zake ndi nyemba basi. Wachiwiri wa Student Union Council pa sukulupo a Tiyanjane Chisowire wati ndiwodandaula chifuwa ma sabata akwana anayi tsopano chitsegulire sukuluyi koma ndiwo zimangokhala nyemba basi. Mtsogoleri wa sukuluyi […]
The post Ana sukulu pa Soche Technical achita ziwonesero kamba ati akungodya nyemba basi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.