Ku Kasungu, mnyamata wa zaka zisanu ndi zitatu (8) ndi mchimwene wake wa zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi (16) afa pamene bambo awo ndi mwana wina agonekedwa mchipatala atadya kalongonda kamba ka vuto lakusowa chakudya. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Kasungu a Joseph Kachikho omwe ati nkhaniyi yachitika m’mudzi mwa […]
The post Ana awiri abanja limodzi afa atadya kalongonda appeared first on Malawi 24.