Amwene, ndapita – Mwenifumbo watuluka UTM

Watsatira Winiko, naye kudzisiya. Amene anali mneneri wa chipani cha UTM, a Frank Mwenifumbo, atsanzika kwa mtsogoleri wa chipanichi, a Saulos Chilima. Malinga ndi chikalata chimene Malawi24 yaona, a Mwenifumbo ati iwo atula pansi udindo wawo ndinso atuluka chipani cha mu boma cha UTM. “Ndaona kuti ndikapange zina, ndayamba ndapuma ku ndale,” alemba motelo a […]

The post Amwene, ndapita – Mwenifumbo watuluka UTM appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください