Amila ndi kumwalira akufuna kuba nsomba mumisampha ya eni ku Mangochi

Zachitika ku Mangochi pamene bambo wa zaka 30 wamwalira atamila panthawi yomwe amafuna kuba Msomba mu misampha ya asodzi anzake. Mneneli wapolisi ya Mangochi Amina Tepani Daudi watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti mkuluyu ndi Issah Kamwendo ochokera m’mudzi mwa Namasiyano mfumu yaikulu Chimwala m’boma la Mangochi lomweli. Malipoti ati pa 26 February 2024, mkuluyu adazemba […]

The post Amila ndi kumwalira akufuna kuba nsomba mumisampha ya eni ku Mangochi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください