‘Amene anatha ndiamene anamwalira munthu samatha ali moyo’- watero Chipiliro Mwancheka

Oyimba Chipiliro Mwancheka wati iye sanathe ndipo atulutsa chimbale chatsopano chotchedwa ‘Ndabwera’ posachedwa. Chimbale chatsopano chimene akuyembekezera kutulutsa muli nyimbo zokwanira khumi ndipo zonse wayimba yekha. Nyimbo zisanu ndi zitatu wajambula yekha ku studio kwake pomwe ziwiri zajambulidwa ndi Viwe Chibwana, Dj Lobodo mothandizana ndi Banderous. Mwancheka wanenanso kuti nyimbo za tsopanozi waphatikizamo makhirikhiri chifukwa […]

The post ‘Amene anatha ndiamene anamwalira munthu samatha ali moyo’- watero Chipiliro Mwancheka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください