“Hallo, ndapatsidwa ndalama yokwana K500,000 ndi m’bale wanu kuti ndikutumizileni, nde kuti ikufikeni munditumizile kaye K50,000”: Amayi awiri ochanuka m’maso adzikapatsilidwa nsima pa zenera ku polisi ya Zomba chifukwa chofuna kulowetsa ma simu kadi okwana 68 mwachinyengo ku ndende yaikulu ya Zomba. Watsimikiza za nkhaniyi ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya Zomba a […]
The post Amayi awiri akwidzingidwa pofuna kulowetsa ma sim card 68 ku ndende ya Zomba appeared first on Malawi 24.