Apolisi ku Nathenje, Lilongwe amanga mayi wa zaka 25 a Ivy Elinati komanso mamuna wake wa zakanso 25, a Mphatso Nalinde, powaganizira kuti adapotokola khosi nkupheratu, mwana wawo wa zaka ziwiri pofuna kukhwima kuti alemere. Mneneri wa polisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu ati a Elinati ndi mayi wa mwanayo ndipo a Nalinde anali bambo […]
The post Amangidwa popotokola khosi la mwana wawo pofuna kukhwima kuti alemere appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.