Apolisi ku Lilongwe amanga a Thokozani Charles, powaganizira kuti adaba mafoni awiri a mayi wina atamunamiza kuti amukwatira komanso kuti alemera akachita zizimba. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati mkuluyu, yemwe amachita malonda ogulitsa zovala, adakumana ndi mayiyo pa tsamba la mchezo la Facebook sabata ziwiri zapitazo. Kenaka akuti adakakumana ku malo […]
The post Amangidwa pobera mkazi mafoni atamunamiza kuti amukwatira, komanso alemera ndichizimba appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.