AMalawi mumva kuwawa – Chakwera

Pulezidenti wa dziko lino Lazarus Chakwera wati aMalawi amva kuwawa kwa miyezi ikubwerayi potsatira kugwa mphamvu kwa ndalama ya Kwacha. A Chakwera ananena izi usiku wa lachitatu pomwe amayankhula kwa mtundu wa aMalawi kuchokera ku nyuma ya ufuma ya Kamuzu. A Chakwera anakumbutsa aMalawi kuti m’mene ankalumbiritsidwa mu chaka cha 2020 ananena kale kuti kukonzaso […]

The post AMalawi mumva kuwawa – Chakwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください