Unyinji unakhamukira ku Njamba lamulungu lija ati si chifukwa chokonda a Mutharika, kapena DPP, kapena kukhumudwa ndi kayendetsedwe ka dziko kamba ka utsogoleri wa Tonse. Ati vuto la onse aja ndi umbuli basi, monga amakhalira a Malawi ochuluka. A Chawezi Banda omwe ndi muwulutsi pa wailesi ya kanema ya Mibawa ndiwo anena izi. Iwo amayankhula […]
The post Amalawi ambiri ndi mbuli – watero muwulutsi wa pa Mibawa Chawezi Banda appeared first on Malawi 24.