Amai 56 a Bungwe la Catholic Women Organization (CWO) ochokera mu Diocese ya Zomba anyamuka Lachiwiri madzulo kupita ku Mzuzu Diocese komwe akukhala nawo pa msonkhano wa pachaka wa amai a Bungweli wochokera ma Diocese onse muno Malawi. Poyankhula asadanyamuke ku Zomba Cathedral yemwe adayimilira wapampando wa bungwe la CWO mu Diocese ya Zomba Professor […]
The post Amai a CWO mu Diocese ya Zomba akakhala nawo pa msonkhano wa pachaka ku Mzuzu appeared first on Malawi 24.