Aliyense atengepo mbali polimbana ndi ziphuphu ndi katangale – Chizuma

Mkulu wa bungwe lolimbana ndi kuthana ndi mchitidwe wa ziphuphu komanso katangale  la Anti-corruption Bureau, mai Martha Chizuma, ati ndi kofunika kugwirana manja kuti dziko lino lipambane pa nkhondo yolimbana ndi mchitidwe oipawu. A Chizuma amayankhula izi dzulo pomwe bungwe la ACB mogwilizana ndi khonsolo ya boma la Balaka linakonza mwambo osesa komanso kuchotsa zinyalala […]

The post Aliyense atengepo mbali polimbana ndi ziphuphu ndi katangale – Chizuma appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください