Alimi samalani: Bambo amunjata kamba kogulitsa feteleza wachinyengo

Apolisi ku Kasungu amanga a James Phiri a zaka 36 zakubadwa kamba kopezeka akugulitsa zinthu zonga ngati feteleza zomwe anazipakira m’matumba a feteleza ndikumagulitsa ngati feteleza. Mkuluyu wamangidwa dzulo kutsatira anthu ena omwe anatsina khutu a polisi pa zankhaniyi ndipo anachita kafukufuku mtauni ya Kasungu ku shopu ya mkuluyu ndipo anapezadi feteleza wachinyengoyu atapakilidwa m’matumba […]

The post Alimi samalani: Bambo amunjata kamba kogulitsa feteleza wachinyengo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください