Alimi m’dziko muno awalangiza kuti azibzala mbeu zosiyanasiyana ngatu njira imodzi yothana ndi vuto losowa chakudya chokwanira komaso kusintha kwa nyengo. Mkulu wa Lilongwe District Agriculture Extension Coordinating Committee (DAECC) Akunsitu Kananji ndiye anayankhula izi pa tsiku la alangizi a za ulimi mu mzinda wa Lilongwe ndipo walimbikitsa alimi kubzala mbeu zosiyanasiyana ngati njira imodzi […]
The post Alimi awalangiza kuti azibzala mbeu zosiyanasiyana appeared first on Malawi 24.