Alimi achenjezedwa zogula feteleza wa manyowa pa nsika

Potsatira kukwera mtengo kwa feteleza wa mankhwala yemwe pano thumba lolemera 50 kilogalamu likugulitsidwa pa mtengo osachepera K90,000 m’malo ena, alimi achenjezedwa kuti asamalitse kwambiri akamagula feteleza opangidwa kuchokera ku manyowa yemwe ali mbwee m’misika pa mitengo yotsikirapo. Ngakhale kuti dziko lino lilibe miyezo yoyenera yopangira feteleza kuchokera ku manyowa, malonda a feteleza wachilengedweyu afala […]

The post Alimi achenjezedwa zogula feteleza wa manyowa pa nsika appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください