Alimi a mdera la Zomba Malosa adandaula kuti mpaka pano sadagulebe fetereza wobereketsa wa Urea ndipo awopseza kuti pofika lachiwiri ngati akhale asadagule achita chothekera kuti akafike kumalo omwe amapangira fetereza ndikukachita ziwonetsero. M’modzi mwa alimi ochokera mdera la Zomba Malosa a Lanjesi Saizi auza Malawi24 kuti tsopano chikhulupiliro chawathera chokuti akhala ndi mwai ogula […]
The post Alimi a Zomba Malosa adandaula kuti sadagulebe fetereza wobereketsa appeared first on Malawi 24.