Chikomekome chamkuyu… Ngati alipo anthu akugomelabe utsogoleri wa Chakwera ndiye ndi kutheka ndi a pa banja pawo ndi nduna zawe zokha basi. Mwina ndi a Yufi owelegeka. Chifukwa kafukufuku waonetsa kuti pa a Malawi handede alionse, khumi okha ndiwo akupatsidwa chilimbikitso cha mphamvu ndi utsogoleri wa abusa a Chakwera. Malinga ndi zotsatila za kafukufuku amene […]
The post Alibe moto Chakwera, anthu atopa naye – atelo a Katswiri a kafukufuku appeared first on Malawi 24.