Ali mchitokosi kamba kochitira chiwembu wakabaza wa njinga yamoto

Apolisi ku Limbe mumzinda wa Blantyre akusunga mchitokosi bambo wina wa zaka 34 pamene iye ndi azake ena anayi anachitira chiwembu munthu wina woyendetsa njinga yamoto yakabaza ya mtundu wa Lifan LF 150-7 yomwe nambala yake ndi BT 12854 ndicholinga chofuna kumubera. Nkhani yonse ikuti bamboyu yemwe dzina lake ndi Bright Maisa anagwilizana ndi mwini […]

The post Ali mchitokosi kamba kochitira chiwembu wakabaza wa njinga yamoto appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください