Akweza madzi ku Blantyre

Ngati simufa ndi njala, ndiye mwina ludzu kapena kolera zitha kukuphani. A bungwe la Blantyre Water Board alengeza kuti madzi awo akwera mtengo. Mu chikalata chimene bungweli latulutsa, a boma tsopano awapatsa chilolezo choti madzi akwere. Iwo ati madziwa akwera kuyambira pa 1 April, kutanthauza kuti pamapeto pa Mwezi uno ma bilu amene abwere akhala […]

The post Akweza madzi ku Blantyre appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください