Mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG), Prophet Shepherd Bushiri, wachenjeza anthu omwe akumema anthu m’masamba amchezo kuti apite munsewu kukachita zionetsero pofuna kukakamiza Mneneriyu kuti apikisane nawo pa udindo wa pulezidenti pa chisankho chapatatu chomwe chichitike chaka cha mawa m’dziko muno, ponena kuti asachite zoterezi popeza ndizosephana ndi chifuniro chawo. A Bushiri anena […]
The post Akundikakamiza kuti ndipikisane nawo pa mpando wa upulezidenti, ndizotsutsana ndi chifuniro changa–Bushiri appeared first on Malawi 24.