Akhristu a Mpingo wa Katolika ku St Charles Lwanga Parish komanso akhristu a mpingo wa Anglican ku St George’s Parish mu mzinda wa Zomba lero ayenda njira yamtanda mogwirizana pokumbukira imfa ya Yesu Khristu. Njira yamtandayi idayambira ku St George’s Anglican Parish mpaka kukafika ku St Charles Lwanga Roman Catholic Church ndipo idatsogodzedwa ndi a […]
The post Akhristu a St Charles Lwanga ndi St George ayenda njira yamtanda mogwirizana appeared first on Malawi 24.