Akatswiri pa malimidwe alimbikitsa kuteteza nthaka ndi zachilengedwe

Akatswiri pa za malimidwe atsindika pa kufunikira koteteza nthaka kuti alimi azikolora chakudya chokwanira. Mkulu oyendetsa polojekiti ya Adaptation Fund a Gilbert Kapunda ati kuguga kwa nthaka kuphatikizanso kusintha kwa nyengo kwakhudza kwambiri ntchito za ulimi mu dziko lino zomwe zapangitsa kuti alimi asamakolore zochuluka. Polojekiti ya Adaptation Fund yomwe cholinga chake ndi kulimbikitsa kuteteza […]

The post Akatswiri pa malimidwe alimbikitsa kuteteza nthaka ndi zachilengedwe appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください