Akakhala ku ndende kwa zaka zitatu kamba kochitira nkhanza mwana omupeza

Bwalo la majesitireti m’boma la Mangochi lagamula Martha Victor a zaka 32 zakubadwa kukhala ku ndende kwa zaka zitatu chifukwa chovulaza mwa omupeza kamba koti anakodzera nyumba. Malinga ndi mboni ya boma, Ted Namaona wati mayi victor anakwatirana ndi bambo wa mwanayi zaka zinayi zapitazo ndipo bamboyu amagwira ntchito m’boma la Chiradzulu kotero amayendera banja […]

The post Akakhala ku ndende kwa zaka zitatu kamba kochitira nkhanza mwana omupeza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください