Akaidi ku Kasungu lero akumbukila maufulu achibadwidwe

Akaidi pa ndende ya Kasungu lero pa 5 December anali pa mwambo okumbukira ufulu wa chibadwidwe pa mutu woti “Ulemu, Ufulu ndi Chilungamo kwa Onse.” Ndipo ngati njira imodzi yofalitsira uthengawu, iwo anagwiritsa ntchito maluso osiyanasiyana pa mwambowu. Kudzera musewero lomwe  iwo anachita, iwo ati anthu ochuluka amamangidwa ndikugamulidwa kukaseweza ndende ngakhale kuti anali ndi […]

The post Akaidi ku Kasungu lero akumbukila maufulu achibadwidwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください