Agwidwa ndi bomba pomwe amafuna kukalithira nsika

Anyamata awiri akusungidwa mchitokosi cha apolisi ku Mwanza atagwidwa ndi bomba pa malo ochitira chipikisheni munsewu wa Mwanza-Blantyre pomwe iwo anali pa ulendo wawo okalithira nsika bombali. A Hope Kasakula yemwe ndi wofalitsa nkhani pa polisi ya mwanza wati anyamata awiriwa ndi a Andrew Gauti Stephano azaka 31 ndi a Justin Lewis azaka 30. Kasakula […]

The post Agwidwa ndi bomba pomwe amafuna kukalithira nsika appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください