Agamulidwa kukakhala ku ndende kaamba koseweletsa maliseche a msungwana wachichepere

Bwalo la milandu ku Balaka, lagamula bambo wa zaka 59 zakubadwa a Steven Finye kukakhala ku ndende komanso kugagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka ziwiri kaamba kopezeka olakwa pa mlandu oseweletsa maliseche a msungwana wa zaka zisanu ndi zinayi (9). Malingana ndi chikalata chochokera ku Polisi ya Balaka chomwe wasainila ndi wachiwiri kwa ofalitsa […]

The post Agamulidwa kukakhala ku ndende kaamba koseweletsa maliseche a msungwana wachichepere appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください