Pena munthu ukaganiza kwambiri ukumati mwina bolaso kuweta agalu athu omwewa achikudawa. Komabe kuganiza izi ndi kamba kamkwiyo nde tiyeni tizisiye naye zimenezo, koma funso nkumati alira bwanji makolo ake a Miracle omwe amawona tsogolo lokoma mwa mwana wawo Miracle. Nanga anzake adziti chiyani kwenikweni pomwe atangomaliza kusewera phada komaso fish-fish limodzi, dzuwa lisanalowe awuzidwa […]
The post Agalu achizungu alikhwira ndi kupha mwana appeared first on Malawi 24.