Anthu akudera la mfumu yaikulu Mtumbwinda m’boma la Machinga, akukhala mwa mantha kamba ka afisi olusa omwe akuti kumayambiliro a mwezi uno apha munthu m’modzi komaso loweluka lapitali avulazaso munthu wina. Yatsimikiza za nkhaniyi ndi mfumu yaikulu Mtumbwinda yomwe inabadwa Franklin Chikwewu Chome yomwe yati nyama zolusazi zinayamba kalekale kuvutitsa kudera lakeli. Mfumu ya ndodoyi […]
The post Afisi avuta kwambiri ku Machinga appeared first on Malawi 24.