Mukamva ena akupitirira kunena kuti agona pa filling station chifukwa amasaka mafuta, adziweni ndi opanda chilungamo chabe. Mafuta analonjezedwa kufika lero aja tsopano afika. Ngambwi ngambwi, a Chakwera sakucheza. Patatha sabata a Malawi atazunzika ndi kusowa kwa mafuta, mafuta ochuluka kwambiri afika mu dziko muno lero lolemba. Izi ndi malingana ndi Malipoti a nyumba zina […]
The post Afika tsopano mafuta ngambwi ngambwi aja appeared first on Malawi 24.