Kuganiza bwino ankanena wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ndikutheka si pa ndale pokha, mwinanso kuchenjela manja kumene. Malipoti ochokela mu dziko la United Kingdom asonyeza kuti a Saulos Chilima ali pa mndandanda wa anthu amene akukayikilidwa kuti akhala akulandila ziphuphu kwa mkulu okayikilidwa za katangale a Zuneth Sattar. Malinga ndi malipoti amene anayalidwa mu […]
The post ‘Afana otani?’ a Chilima, a Chimwendo, a Matemba ndi ena awatchula pa mndandanda wa okudya za Sattar appeared first on Malawi 24.