Adindo ena pa msika wa Namadzi ku Chiradzulu adandaula ndikusowa kwa zipangizo zochotsela zinyalala monga mawilibala ndi mafosholo pamsikawu. A George Mkwate m’modzi, wa mamembala a komiti pamsikawu wati mawilibala, mafosholo komanso zotchinga kukamwa ndi zina mwa zinthu zomwe alibiletu pamsikawu. “Kusowa kwa zinthu zimenezi kumaika moyo wathu pa chiopsezo cha matenda osiyanasiyana,” adatero a […]
The post Adindo adandaula ndikusowa kwa zipangizo zochotsela zinyalala pa msika wa Namadzi appeared first on Malawi 24.