Boma latsimikiza kuti gulu la chiwiri la achinyamata okwana 200 linyamuka m’dziko muno lachitatu kupita kukagobola ntchito zakumunda m’dziko la Israel. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani ku unduna wazantchito a Nellie Kapatuka omwe awuza nyumba zina zofalitsa nkhani m’dziko muno kuti ndege yomwe ikuyembekezeka kunyamula anthuwa, ifika m’dziko muno lero lachiwiri masana ano Malingana […]
The post Achinyamata ena 200 wapsa wa ku Israel mawa appeared first on Malawi 24.