Achinyamata adandaula ndi zachinyengo pa pulojekiti ya USAID ku Chiradzulu

Magulu a achinyamata m’boma la Chiradzulu apempha Bwanankubwa wa bomali kuti aimitse ndondomeko yosankha achinyamata oti achite maphunziro azamalonda pansi pa bungwe la USAID ponena kuti pachitika zachinyengo pa ndondomekoyi. Malinga ndi kalata yomwe maguluwa alemba yomwe yasainidwa ndi Macfallen Monjeleriwa, ati ndi zodabwitsa kuti achinyamata  asiyidwa kumbali pamene pamayambiliro a pulojeketiyi anauzidwa kuti atenga […]

The post Achinyamata adandaula ndi zachinyengo pa pulojekiti ya USAID ku Chiradzulu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください