Achinyamata a ulendo wopita ku Israel akukachita M’bindikiro ku capital Hill

Achinyama 4,000 amene anakonza ziphaso zawo ndi ndondomeko zonse kuyembekezera kunyamuka ulendo okagwira ntchito ku minda mdziko la Israel, ati lero akumana pa manda a Kamuzu pa ulendo wawo wokachita m’bindikiro ku ma ofesi aboma, kudandaulira ofesi ya mtsogoleri wa dziko ndi nduna (OPC) mu Mzinda wa Lilongwe. M’malingana ndi m’modzi mwa achinyamata omwe Malawi24 […]

The post Achinyamata a ulendo wopita ku Israel akukachita M’bindikiro ku capital Hill appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください