Achinyamata 140 akupita ku Israel mawa

Achinyamata okwana 140 akuyembekezeka kunyamuka m’dziko muno mawa kupita ku Israel komwe akukagwira ntchito ku minda. Achinyamatawa omwe afika kale Ku Kamuzu International Airport akhala akunyamuka m’bandakucha wa lachitatu. Polankhula ndi Malawi24, mkulu wa kampani yomwe ikutumiza achinyamata yotchedwa Arava Farmers Agency a Justice Kangulu anena kuti achinyamatawa akukagwira ntchito zosiyanasiyana ku minda ya ku […]

The post Achinyamata 140 akupita ku Israel mawa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください